HTML5 55
Untitled Guest on 21st July 2020 10:25:35 PM
 1. <body bgcolor="skyblue" >
 2. <h1>MIZIMBAYITSO</h1>
 3.  
 4.  
 5. <li><b>Mzimbayitso </b>ndi mawu onena nkhani mopanda chindunji; kapena tinene kuti
 6. mophiphiritsa.</li>
 7. <br>
 8. <h3> Mizimbayitso ilipo yosiyanasiyana ndipo ina mwa iyo ndi iyi:</h3>
 9.  
 10.  
 11. <b>(a)  Mizimbayitso yonyoza</b>
 12.  
 13. <li>Iyi ndi mizimbayitso ya matanthauzo onyoza.</li>
 14. <br>
 15. <li> Poyankhula munthu
 16. amachita ngati akuyamikira, pomwe m'maganizo ake muli kunyogodola
 17. kapena kuyipitsa.</li>
 18.  
 19. <h4>Zitsanzo:</h4>
 20.  
 21.  
 22. <table border="1" >
 23.  
 24. <tr>
 25. <th>Mzembaitso</th><th>Tanthauzo</th>
 26. </tr>
 27. <tr>
 28. <td>Chisotichi chakukhala bwino</td>
 29.  <td>kuyamikira monama pamene
 30. munthuyo chisoticho
 31. sichidamukhale bwino</td></tr>
 32. <tr><td>
 33. Koma ndiye ndiwozi wazikazinga bwino kwambiri</td><td>kuyamikira monama
 34. pamene ndiwozo
 35. sadakazinge bwino
 36. </td></tr>
 37.  
 38. <br>
 39. <b>(b)  Mizimbayitso yonyalapsa</b>
 40. <br>
 41. <br>
 42. <li>Mawu onyalapsa amanenedwa ndi cholinga chopereka ulemu kapena
 43. kuchepetsa nthumanzi kapenanso mantha omwe munthu ali nawo.</li>
 44. <br>
 45. <br>
 46. <li>Munthu amanena mwaulemu kapena mosafuna kutchula mawu omwe
 47. akhoza kusonyeza ngati mawu achipongwe kapena opanda ulemu
 48. kapena otukwana kapenanso ochititsa phuma.
 49. </li>
 50. <br>
 51. <b>Zitsanzo:</b>
 52. <br>
 53.  
 54. <table border="1" > <tr>
 55. <th>Mizimbayitso yonyalapsa</th><th>Tanthauzo</th></tr>
 56.  
 57. <tr>
 58. <td> Abambo aja atisiya</td><td>Abambo amwalira</td>
 59. </tr>
 60.  
 61. <tr>
 62. <td>Mwana wapambuka</td> <td>Mwana wanyera kapena wasoma.</td>
 63. </tr>
 64. <tr>
 65. <td>Mwana wayipitsira pano</td> <td>Mwana wanyera kapena wasoma.</td></tr>
 66.  
 67. <tr>
 68. <td> Ndifuna ndikataye madzi</td> <td>Ndifuna ndikakodze.</td>
 69. </tr>
 70.  
 71. <tr>
 72. <td> Ndinapita kukayimirira</td><td>Ndinakakodza.</td></tr>
 73. <tr>
 74. <td>Nambewe ngodwala</td> <td>Nambewe akuyembekezera kubala
 75. mwana.</td></tr>
 76. <tr>
 77. <td>Mkaziyu ngoyendayenda</td><td>Mkaziyu ndi wachiwerewere, hule
 78. kapena wadama.</td></tr>
 79. <tr>
 80. <td> Mnyamata chamuyambwa chitedze</td><td>Mnyamata watenga nthenda
 81. chifukwa cha chiwerewere.</td></tr>
 82.  
 83. <tr>
 84. <td> Mayiyu wapita padera</td> <td>Mayiyu wabala mwana wakufa.</td>
 85. </tr>
 86. <tr>
 87. <td> Mtsikanayu ali ndi pakati</td><td>Mtsikanayu ali ndi mimba.</td>
 88. </tr>
 89. </body>
 90.  
 91.  
 92.  
 93.  
 94. <marquee>Developed by Welford Khodo Kuthakwaanthu </marquee>

Paste is for source code and general debugging text.

Login or Register to edit, delete and keep track of your pastes and more.

Raw Paste

Login or Register to edit or fork this paste. It's free.